Daniel 4:29 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Itatha miyezi khumi ndi iwiri, analikuyenda m'chinyumba chachifumu cha ku Babiloni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Itapita miyezi khumi ndi iwiri, pamene mfumu inkayenda pa denga la nyumba ya ufumu ya ku Babuloni,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Itatha miyezi khumi ndi iwiri, analikuyenda m'cinyumba cacifumu ca ku Babulo.