Daniel 4:3 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ha! Zizindikiro zake nzazikulu, ndi zozizwa zake nza mphamvu, ufumu wake ndiwo ufumu wosatha, ndi kulamulira kwake ku mibadwomibadwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zizindikiro zake ndi zazikulu, zozizwitsa zake ndi zamphamvu! Ufumu wake ndi wamuyaya; ulamuliro wake ndi wa mibadomibado.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ha! zizindikilo zace nzazikuru, ndi zozizwa zace nza mphamvu, ufumu wace ndiwo ufumu wosatha, ndi kulamulira kwace ku mibadwo mibadwo.