Daniel 4:30 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mfumu inanena, niti, Suyu Babiloni wamkulu ndinammanga, akhale pokhala pachifumu, ndi mphamvu yanga yaikulu uoneke ulemerero wa chifumu changa?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
iye anati, “Kodi Babuloni si mzinda wamphamvu ndi wokongola umene ndinamanga ndi mphamvu zanga ngati nyumba yanga yaufumu, kuonetsera ulemerero wa ufumu wanga?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mfumu inanena, niti, Suyu Babulo wamkuru ndinammanga, akhale pokhala pacifumu, ndi mphamvu yanga yaikuru uoneke ulemerero wa cifumu canga?