Daniel 4:31 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akali m'kamwa mwa mfumu mau awa, anamgwera mau ochokera kumwamba, ndi kuti, Mfumu Nebukadinezara, anena kwa iwe: ufumu wakuchokera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akuyankhulabe izi mawu anamveka kuchokera kumwamba kuti, “Imvani izi, mfumu Nebukadinezara: Ufumu wako wachotsedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akali m'kamwa mwa mfumu mau awa, anamgwera mau ocokera kumwamba, ndi kuti, Mfumu Nebukadinezara, anena kwa iwe: ufumu wakucokera.