Daniel 4:5 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinaona loto lakundiopsa, ndi zolingirira za pakama panga, ndi masomphenya a m'mtima mwanga, zinandivuta ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndili chigonere pa bedi langa, ndinalota maloto amene anandichititsa mantha. Zinthu ndi masomphenya zimene ndinaziona zinandiopsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinaona loto lakundiopsa, ndi zolingilira za pakama panga, ndi masomphenya a m'mtima mwanga, zinandibvuta ine.