Daniel 4:6 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake ndinalamulira kuti adze kwa ine anzeru onse a ku Babiloni, kuti andidziwitse kumasulira kwake kwa lotoli.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho ndinalamula kuti anthu onse a nzeru a ku Babuloni abwere pa maso panga kunditanthauzira malotowo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace ndinalamulira kuti adze kwa ine anzeru onse a ku Babulo, kuti andidziwitse kumasulira kwace kwa lotoli.