Daniel 5:2 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Belisazara, pakulawa vinyo, anati abwere nazo zotengera za golide ndi siliva adazichotsa Nebukadinezara atate wake ku Kachisi ali ku Yerusalemu, kuti mfumu ndi akulu ake, akazi ake ndi akazi ake ang'ono, amweremo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene Belisazara ankamwa vinyo, analamula kuti ziwiya zagolide ndi zasiliva zimene Nebukadinezara abambo ake anakatenga mʼNyumba ya Mulungu ku Yerusalemu zikatengedwe kuti mfumu ndi akalonga ake, akazi ake ndi azikazi amweremo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Belisazara, pakulawa vinyo, anati abwere nazo zotengera za golidi ndi siliva adazicotsa Nebukadinezara atate wace ku Kacisi ali ku Yerusalemu, kuti mfumu ndi akuru ace, akazi ace ndi akazi ace ang'ono, amweremo.