Daniel 5:20 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma pokwezeka mtima wake, nulimba mzimu wake kuchita modzikuza, anamtsitsa pa mpando wa ufumu wake, namchotsera ulemerero wake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma pamene inayamba kudzitama ndi kuwumitsa mtima wake ndi kuyamba kunyada, inachotsedwa pa mpando wake waufumu ndi kulandidwa ulemerero wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma pokwezeka mtima wace, nulimba mzimu wace kucita modzikuza, anamtsitsa pa mpando wa ufumu wace, namcotsera ulemerero wace;