Daniel 5:22 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo inu mwana wake, Belisazara inu, simunadzichepetsa m'mtima mwanu, chinkana munazidziwa izi zonse;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Koma inu mwana wake, Belisazara, simunadzichepetse, ngakhale kuti mumadziwa zonsezi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo inu mwana wace, Belisazara inu, simunadzicepetsa m'mtima mwanu, cinkana munazidziwa izi zonse;