Daniel 5:26 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kumasulira kwake kwa mau awa ndi uku: MENE, Mulungu anawerenga ufumu wanu, nautha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Zimene mawuwa akutanthauza ndi izi: Mene: Mulungu wawerenga masiku a ufumu wanu ndipo wauthetsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kumasulira kwace kwa mau awa ndi uku: MENE, Mulungu anawerenga ufumu wanu, nautha.