Daniel 5:29 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Belisazara analamulira, ndipo anaveka Daniele chibakuwa, ndi unyolo wagolide m'khosi mwake, nalalikira za iye kuti ndiye wolamulira wachitatu m'ufumumo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwa lamulo la Belisazara, Danieli anavekedwa chovala cha pepo, mkanda wagolide unayikidwa mʼkhosi mwake, ndipo analengeza kuti anali wachitatu mu ulamuliro mu ufumuwo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Belisazara analamulira, ndipo anabveka Danieli cibakuwa, ndi unyolo wagolidi m'khosi mwace, nalalikira za iye kuti ndiye wolamulira wacitatu m'ufumumo.