Daniel 5:31 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Dariusi Mmedi analandira ufumuwo ali wa zaka makumi asanu ndi limodzi mphambu ziwiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo Dariyo Mmedi analanda ufumuwo ali ndi zaka 62.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Dariyo Mmedi analandira ufumuwo ali wa zaka makumi asanu ndi limodzi mphambu ziwiri.