Daniel 5:4 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anamwa vinyo, nalemekeza milungu yagolide, ndi yasiliva, yamkuwa, yachitsulo, yamtengo, ndi yamwala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akumwa vinyo, anatamanda milungu yagolide ndi siliva, yamkuwa, chitsulo, yamtengo ndi mwala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anamwa vinyo, nalemekeza milungu yagolidi, ndi yasiliva, yamkuwa, yacitsulo, yamtengo, ndi yamwala.