Daniel 6:1 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kudamkomera Dariusi kuikira ufumuwo akalonga zana limodzi mphambu makumi awiri akhale m'madera onse a ufumu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kunamukomera Dariyo kusankha akalonga 120 kuti alamulire mu ufumu wonse,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kudamkomera Dariyo kuikira ufumuwo akalonga zana limodzi mphambu makumi awiri akhale m'madera onse a ufumu;