Daniel 6:19 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nilawira mamawa mfumu, nimuka mofulumira kudzenje la mikango.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼbandakucha, mfumu inanyamuka ndi kufulumira kupita ku dzenje la mikango lija.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nilawira mamawa mfumu, nimuka mofulumira ku dzenje la mikango.