Daniel 6:27 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iye apulumutsa, nalanditsa, nachita zizindikiro ndi zozizwa m'mwamba ndi pa dziko lapansi, ndiye amene anapulumutsa Daniele kumphamvu ya mikango.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amalanditsa ndipo amapulumutsa, amachita zizindikiro ndi zozizwitsa kumwamba ndi pa dziko lapansi. Iye walanditsa Danieli ku mphamvu ya mikango.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iye apulumutsa, nalanditsa, nacita zizindikilo ndi zozizwa m'mwamba ndi pa dziko lapansi, ndiye amene anapulumutsa Danieli ku mphamvu ya mikango.