Daniel 7:12 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo zilombo zotsalazo anazichotsera ulamuliro wao, koma anatalikitsa moyo wao, ukhalenso nyengo ndi nthawi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zirombo zina zija zinalandidwa ulamuliro wawo, koma zinaloledwa kukhala ndi moyo kwa kanthawi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo zirombo zotsalazo anazicotsera ulamuliro wao, koma anatalikitsa moyo wao, ukhalenso nyengo ndi nthawi.