Daniel 7:15 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ine Daniele, mzimu wanga unalaswa m'kati mwa thupi langa, ndi masomphenya a m'mtima mwanga anandivuta.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ine Danieli ndinavutika mu mzimu, ndipo zimene ndinaziona mʼmasomphenya zinandisautsa mʼmaganizo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ine Danieli, mzimu wanga unalaswa m'kati mwa thupi langa, ndi masomphenya a m'mtima mwanga anandibvuta.