Daniel 7:16 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinayandikira kwa wina wa iwo akuimako ndi kumfunsa za choonadi za ichi chonse. Ndipo ananena nane, nandidziwitsa kumasulira kwake kwa zinthuzi:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinayandikira mmodzi mwa amene anayima pamenepo ndi kumufunsa tanthauzo lenileni la zonsezi. “Kotero anandiwuza ndi kundipatsa tanthauzo la zinthu zonse izi:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinayandikira kwa wina wa iwo akuimako ndi kumfunsa za coonadi za ici conse. Ndipo ananena nane, nandidziwitsa kumasulira kwace kwa zinthuzi: