Daniel 7:17 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zilombo zazikulu izi zinai ndizo mafumu anai amene adzauka pa dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
‘Zirombo zikuluzikulu zinayi zija ndi maufumu anayi amene adzaoneka pa dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zirombo zazikuru izi zinai ndizo mafumu anai amene adzauka pa dziko lapansi.