Daniel 7:18 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma opatulika a Wam'mwambamwamba adzalandira ufumuwo, ndi kukhala nao ufumu kosatha, kunthawi zonka muyaya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma oyera mtima a Wammwambamwamba adzalandira ufumu ndipo udzakhala nawo mpaka muyaya, inde ku nthawi zonse.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma opatulika la Wam'mwambamwamba adzalandira ufumuwo, ndi kukhala nao ufumu kosatha, ku nthawi zomka muyaya.