Daniel 7:21 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinapenya, ndipo nyanga yomweyi inachita nkhondo ndi opatulikawo, niwalaka, mpaka inadza Nkhalamba ya kale lomwe;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikuyangʼanitsitsa, nyanga imeneyi inathira nkhondo anthu oyera mtima ndi kuwagonjetsa,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinapenya, ndipo nyanga yomweyi inacita nkhondo ndi opatulikawo, niwalaka, mpaka inadza Nkhalamba ya kale lomwe;