Daniel 7:24 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kunena za nyanga khumi, m'ufumu uwu adzauka mafumu khumi, ndi pambuyo pao idzauka ina; iyo idzasiyana ndi oyamba aja, nidzachepetsa mafumu atatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nyanga khumi zija ndiwo mafumu khumi amene adzatuluka mu ufumu umenewu. Pambuyo pake mfumu ina idzadzuka, yosiyana ndi mafumu a mʼmbuyomu; iyo idzagonjetsa mafumu atatu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kunena za nyanga khumi, m'ufumu uwu adzauka mafumu khumi, ndi pambuyo pao idzauka yina; iyo idzasiyana ndi oyamba aja, nidzacepetsa mafumu atatu.