Daniel 8:1 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chaka chachitatu cha Belisazara mfumu masomphenya anandionekera kwa ine Daniele, atatha kundionekera oyamba aja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chaka chachitatu cha ulamuliro wa mfumu Belisazara, Ine Danieli, ndinaonanso masomphenya, ena atatha amene anandionekera poyamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Caka cacitatu ca Belisazara mfumu masomphenya anandionekera kwa ine Danieli, atatha kundionekera oyamba aja.