Daniel 8:18 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo m'mene analikulankhula ndi ine ndinagwidwa ndi tulo tatikulu, nkhope yanga pansi; koma anandikhudza, nandiimiritsa pokhala inepo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene ankandiyankhula ndinadzigwetsa pansi chafufumimba, nʼkugona tulo tofa nato. Kenaka anandikhudza ndi kundiyimiritsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo m'mene analikulankhula ndi ine ndinagwidwa ndi tulo tatikuru, nkhope yanga pansi; koma anandikhudza, nandiimiritsa pokhala inepo,