Daniel 8:2 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinaona m'masomphenya; tsono kunali, pakuwaona ine ndinali m'Susa, m'nyumba ya mfumu, ndiwo m'dziko la Elamu; ndinaona m'masomphenya kuti ndinali kumtsinje Ulai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinaona mʼmasomphenya kuti ndinali mu mzinda wotetezedwa wa Susa mʼchigawo cha Elamu. Mʼmasomphenyawo ndinaona nditayima pafupi ndi mtsinje wa Ulai.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinaona m'masomphenya; tsono kunali, pakuwaona ine ndinali m'Susani, m'nyumba ya mfumu, ndiwo m'dziko la Elamu; ndinaona m'masomphenya kuti ndinali kumtsinje Ulai.