Daniel 8:20 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nkhosa yamphongo waiona ya nyanga ziwiri ndizo mafumu a Mediya ndi Persiya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nkhosa yayimuna ya nyanga ziwiri imene unayiona, ikuyimira mafumu a Amedi ndi Aperezi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nkhosa yamphongo waiona ya nyanga ziwiri ndizo mafumu a Mediya ndi Perisiya.