Daniel 8:21 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi tonde wamanyenje ndiye mfumu ya Agriki, ndi nyanga yaikulu ili pakati pa maso ake ndiyo mfumu yoyamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mbuzi yayimuna ija ndi mfumu ya Agriki, ndipo nyanga yayikulu pakati pa maso ake aja ndi mfumu yoyamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi tonde wamanyenje ndiye mfumu ya Helene, ndi nyanga yaikuru iri pakati pa maso ace ndiyo mfumu yoyamba.