Daniel 8:22 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi kuti zinaphuka zinai m'malo mwake mwa iyo itathyoka, adzauka maufumu anai ochokera mu mtunduwu wa anthu, koma osakhala nayo mphamvu ya uja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kunena za nyanga inathyoka ija ndi nyanga zinayi zimene zinaphuka mʼmalo mwake zikutanthauza maufumu anayi amene adzatuluka mʼdziko lake; koma sizidzafanana mphamvu ndi ufumu woyambawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi kuti zinaphuka zinai m'malo mwace mwa iyo itatyoka, adzauka maufumu anai ocokera mu mtunduwu wa anthu, koma osakhala nayo mphamvu ya uja.