Daniel 8:23 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo potsiriza pake pa ufumu wao, atakwanira olakwa, idzauka mfumu ya nkhope yaukali yakuzindikira zinsinsi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Pa masiku otsiriza a maufumuwa, machimo awo atachulukitsa, padzadzuka mfumu yaukali ndi yochenjera kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo potsiriza pace pa ufumu wao, atakwanira olakwa, idzauka mfumu ya nkhope yaukali yakuzindikira zinsinsi.