Daniel 8:26 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo masomphenya a madzulo ndi mamawa adanenawo ndi oona; koma iwe ubise masomphenyawo, popeza adzachitika atapita masiku ambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Masomphenya okhudza madzulo ndi mmawa amene unawaona aja ndi woona, koma uwasunge masomphenyawa mwachinsinsi popeza ndi onena za masiku a mʼtsogolo kwambiri.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo masomphenya a madzulo ndi mamawa adanenawo ndi oona; koma iwe ubise masomphenyawo, popeza adzacitika atapita masiku ambiri.