Daniel 8:27 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ine Daniele ndinakomoka ndi kudwala masiku ena; pamenepo ndinauka ndi kuchita ntchito ya mfumu; ndipo ndinadabwa nao masomphenyawo, koma panalibe wakuwazindikiritsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine Danieli ndinafowoka ndipo ndinadwala masiku angapo. Kenaka ndinadzuka ndi kupitiriza ntchito za mfumu. Ndinada nkhawa ndi masomphenyawo; ndipo sindinathe kuwamvetsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ine Danieli ndinakomoka ndi kudwala masiku ena; pamenepo ndinauka ndi kucita nchito ya mfumu; ndipo ndinadabwa nao masomphenyawo, koma panalibe wakuwazindikiritsa.