Daniel 8:6 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anadzera nkhosa yamphongoyo yokhala ndi nyanga ziwiri, imene ndidaiona ilikuima kumtsinje, naithamangira ndi mphamvu yake yaukali.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inabwera molunjika nkhosa yayimuna ya nyanga ziwiri ija imene ndinaona itayima pafupi ndi mtsinje. Ndipo inayithamangira mwaukali.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anadzera nkhosa yamphongoyo yokhala ndi nyanga ziwiri, imene ndidaiona irikuima kumtsinje, naithamangira ndi mphamvu yace yaukali.