Daniel 8:9 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mu imodzi ya izi munaphuka nyanga yaing'ono, imene inakula kwakukulu ndithu, kuloza kumwera, ndi kum'mawa, ndi kudziko lokometsetsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa imodzi mwa nyangazo panatuluka nyanga imene inali yocheperapo koma inakula kwambiri kuloza kummwera ndi kummawa ndi kuloza dziko lokongola.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mu imodzi ra izi munaphuka nyanga yaing'ono, imene inakula kwakukuru ndithu, kuloza kumwela, ndi kum'mawa, ndi ku dziko lokometsetsa.