Daniel 9:1 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chaka choyamba cha Dariusi mwana wa Ahasuwero, wa mbeu ya Amedi, amene anamlonga mfumu ya Ababiloni;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼchaka choyamba cha Dariyo mwana wa Ahasiwero (wochokera kwa Amedi), amene anakhala mfumu ya ku Babuloni,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Caka coyamba ca Dariyo mwana wa Ahaswero, wa mbeu ya Amedi, amene anamlonga mfumu ya Akasidi;