Daniel 9:2 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chaka choyamba cha ufumu wake, ine Daniele ndinazindikira mwa mabuku kuti chiwerengo chake cha zaka, chimene mau a Yehova anadzera nacho kwa Yeremiya mneneri, kunena za makwaniridwe a mapasuko a Yerusalemu, ndizo zaka makumi asanu ndi awiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ine Danieli ndinazindikira powerenga mawu a Yehova opatsidwa kwa mneneri Yeremiya, kuti Yerusalemu adzakhala bwinja kwa zaka 70.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
caka coyamba ca ufumu wace, ine Danieli ndinazindikira mwa mabuku kuti ciwerengo cace ca zaka, cimene mau a Yehova anadzera naco kwa Yeremiya mneneri, kunena za makwaniridwe a mapasuko a Yerusalemu, ndizo zaka makumi asanu ndi awiri.