Daniel 9:22 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anandilangiza ine, ndi kulankhula nane, nati, Daniele iwe, ndatuluka tsopano ine kukuzindikiritsa mwaluntha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anandilangiza kuti, “Danieli ndabwera tsopano kuti ndikupatse nzeru kuti uzitha kumvetsa zinthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anandilangiza ine, ndi kulankhula nane, nati, Danieli iwe, ndaturuka tsopano ine kukuzindikiritsa mwaluntha.