Daniel 9:5 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
tachimwa, tachita mphulupulu, tachita zoipa, tapanduka, kupatuka ndi kusiya maneno anu ndi maweruzo anu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
tachimwa ndipo tachita zolakwa ndi zoyipa. Takuwukirani posiya malangizo ndi malamulo anu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
tacimwa, tacita mphulupulu, tacita zoipa, tapanduka, kupambuka ndi kusiya maneno anu ndi maweruzo anu;