Daniel 9:6 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
sitinamvera atumiki anu aneneri, amene ananena m'dzina lanu kwa mafumu athu, akalonga athu, makolo athu, ndi anthu onse a m'dziko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sitinamvere aneneri atumiki anu, amene anayankhula mʼdzina lanu kwa mafumu athu, kwa akalonga athu, makolo athu, ndi kwa anthu onse a mʼdziko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
sitinamvera atumiki anu aneneri, amene ananena m'dzina lanu kwa mafumu athu, akalonga athu, makolo athu, ndi anthu onse a m'dziko.