Daniel 9:8 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ambuye, kwa ife kuli manyazi a nkhope yathu, kwa mafumu athu, kwa akalonga athu, ndi kwa makolo athu; pakuti takuchimwirani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu Yehova, ife ndi mafumu athu, akalonga athu ndi makolo athu tili ndi manyazi chifukwa takuchimwirani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ambuye, kwa ife kuli manyazi a nkhope yathu, kwa mafumu athu, kwa akalonga athu, ndi kwa makolo athu; pakuti takucimwirani.