Deuteronomy 1:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ine ndekha ndingathe bwanji kusenza udindo wokutsogolerani ndi womaweruzanso milandu pakati panu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndikasenza bwanji ndekha kupsinya kwanu, ndi katundu wanu, ndi kulimbana kwanu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma nanga ndekha ndidzasenza bwanji zovuta ndi zipsinjo zanu komanso milandu yanu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndikasenza bwanji ndekha kupsinya kwanu, ndi katundu wanu, ndi kulimbana kwanu?