Deuteronomy 1:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sankhani anthu ena anzeru, omvetsa ndi odziŵa zinthu bwino, pakati pa mafuko anu, ndipo ine ndidzaŵaika kuti akhale atsogoleri pakati panu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Dzifunireni amuna anzeru, ndi ozindikira bwino, ndi odziwika mwa mafuko anu, ndipo ndidzawaika akhale akulu anu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sankhani amuna ena anzeru, ozindikira ndi amene mumawalemekeza kuchokera ku mtundu uliwonse wa mitundu yanu, ndipo ndidzawayika kuti akulamulireni.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Dzifunireni amuna anzeru, ndi ozindikira bwino, ndi odziwika mwa mafuko anu, ndipo ndidzawaika akhale akuru anu.