Deuteronomy 1:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo inu mudaandiyankha kuti, “Zimene mwanenazi nzabwino, ife tidzachitadi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo munandiyankha ndi kuti, Mau mwanenawa ndi abwino kuwachita.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu munandiyankha kuti, “Maganizo amenewa ndi abwino kuwachita.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo munandiyankha ndi kuti, Mau mwanenawa ndi abwino kuwacita.