Deuteronomy 1:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ulendo wa pakati pa Horebu ndi Kadesi-Baranea, kudzera njira ya phiri la Seiri, unali wa masiku 11.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ulendo wake wochokera ku Horebu wofikira ku Kadesi-Baranea, wodzera njira ya phiri la Seiri, ndiwo wa masiku khumi ndi limodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
(Kuyenda kuchokera ku Horebu kukafika ku Kadesi Barinea kudzera njira ya ku Phiri la Seiri ndi ulendo wa masiku khumi ndi limodzi).
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ulendo wace wocokera ku Horebe wofikira ku Kadesi Barinea, wodzera njira ya phiri la Seiri, ndiwo wa masiku khumi ndi limodzi.