Deuteronomy 1:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndidakuuzani kuti, “Tsopano, tafika ku dziko lamapiri la Aamori limene Mulungu wa makolo athu akutipatsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinati kwa inu, Mwafikira mapiri a Aamori, amene Yehova Mulungu wathu atipatsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ndinati kwa inu, “Mwafika ku dziko la mapiri la Aamori, limene Yehova Mulungu wathu akutipatsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinati kwa inu, Mwafikira mapiri a Aamori, amene Yehova Mulungu wathu atipatsa.