Deuteronomy 1:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mau amenewo adandikomera, motero ndidasankha anthu khumi ndi aŵiri, mmodzi pa fuko lililonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo chinandikomera chinthu ichi; ndipo ndinatenga amuna khumi ndi awiri a inu, fuko limodzi mwamuna mmodzi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinaona kuti maganizo amenewa anali abwino, choncho ndinasankha anthu khumi ndi awiri, mmodzi ku fuko lililonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo cinandikomera cinthu ici; ndipo ndinatenga amuna khumi ndi awiri ainu, pfuko limodzi mwamuna mmodzi;