Deuteronomy 1:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adabwerera atatengako zipatso, nafika nazo pakati pathu. Ndipo adatiwuza kuti, “Dziko limene Chauta, Mulungu wathu, akutipatsalo ndi lachonde.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anatengako zipatso za dzikoli m'manja mwao, natsikira nazo kwa ife, natibwezera mau ndi kuti, Dzikoli Yehova Mulungu wathu atipatsa ndi labwino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pobwerera anatitengerako zipatso za mʼdzikomo ndipo anatipatsa mawu akuti, “Dziko limene Yehova Mulungu wathu akutipatsa ndi labwino.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anatengako zipatso za dzikoli m'manja mwao, natsikira nazo kwa ife, natibwezera mau ndi kuti, Dzikoli Yehova Mulungu wathu atipatsa ndi labwino.