Deuteronomy 1:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma inu simudafune kupita, mudaukira ulamuliro wa Chauta, Mulungu wanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma simunafuna kukwerako, ndipo munapikisana nao mau a Yehova Mulungu wanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma inu simunafune kupitako ndipo munawukira lamulo la Yehova Mulungu wanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma simunafuna kukwerako, ndipo munapikisana nao mau a Yehova Mulungu wanu.