Deuteronomy 1:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ine ndidakuuzani kuti, “Musaŵaope anthu amenewo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo ndinati kwa inu, Musamaopsedwa, musamachita mantha nao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ine ndinati kwa inu, “Musachite mantha kapena kuwaopa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo ndinati kwa inu, Musamaopsedwa, musamacita mantha nao.