Deuteronomy 1:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
amene nthaŵi zonse ankatsogola pa ulendo wanu, kuti akupezerenitu malo omangapo mahema anu. Iye ankayenda patsogolo panu m'maonekedwe a moto usiku, kuti akuunikireni njira, koma masana ankakhala ndi maonekedwe a mtambo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
amene anakutsogolerani m'njira, kukufunirani malo akumanga mahema anu ndi moto usiku, kukuonetserani njira yoyendamo inu, ndi mumtambo usana.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
amene anakutsogolerani pa ulendo wanu, ndi moto nthawi ya usiku ndi mtambo nthawi ya masana, kukufunirani malo woti mumange msasa ndi kukuonetsani njira yoti muyendemo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
amene anakutsogolerani m'njira, kukufunirani malo akumanga mahema anu ndi mota usiku, kukuonetserani njira yoyendamo inu, ndi mumtambo usana.